Aefeso 5:27 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 27 Anatero kuti iyeyo alandire mpingowo uli wokongola ndiponso waulemerero,+ wopanda banga kapena makwinya kapenanso chilichonse cha zinthu zotero, koma kuti ukhale woyera ndi wopanda chilema.+ Yuda 24 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 24 Koma ponena za Mulungu amene angathe kukutetezani+ kuti musapunthwe, ndiponso kukuikani opanda chilema+ pamaso pa ulemerero wake ndi chisangalalo chachikulu,
27 Anatero kuti iyeyo alandire mpingowo uli wokongola ndiponso waulemerero,+ wopanda banga kapena makwinya kapenanso chilichonse cha zinthu zotero, koma kuti ukhale woyera ndi wopanda chilema.+
24 Koma ponena za Mulungu amene angathe kukutetezani+ kuti musapunthwe, ndiponso kukuikani opanda chilema+ pamaso pa ulemerero wake ndi chisangalalo chachikulu,