Yeremiya 12:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Abusa ambiri+ awononga munda wanga wa mpesa.+ Apondaponda cholowa changa.+ Cholowa changa chosiririka+ achisandutsa bwinja moti palibe aliyense amene akukhalamo.
10 Abusa ambiri+ awononga munda wanga wa mpesa.+ Apondaponda cholowa changa.+ Cholowa changa chosiririka+ achisandutsa bwinja moti palibe aliyense amene akukhalamo.