Deuteronomo 4:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 “Choncho anthu inu munayandikira ndi kuimirira m’munsi mwa phiri. Phiri limenelo linali kuyaka moto mpaka kumwamba, ndipo kunali mdima ndi mtambo wakuda.+ Chivumbulutso 8:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Ndipo ndinaona ndi kumva chiwombankhanga+ chikuuluka pafupi m’mlengalenga,+ chikulankhula ndi mawu okweza kuti: “Tsoka, tsoka, tsoka+ kwa okhala padziko lapansi, chifukwa cha malipenga otsalawo, amene angelo atatuwo atsala pang’ono kuwaliza!”+ Chivumbulutso 19:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Ndinaonanso mngelo ataimirira padzuwa. Iye anafuula ndi mawu okweza kwa mbalame+ zonse zouluka chapafupi m’mlengalenga, kuti: “Bwerani kuno, dzasonkhaneni ku phwando lalikulu la Mulungu la chakudya chamadzulo,
11 “Choncho anthu inu munayandikira ndi kuimirira m’munsi mwa phiri. Phiri limenelo linali kuyaka moto mpaka kumwamba, ndipo kunali mdima ndi mtambo wakuda.+
13 Ndipo ndinaona ndi kumva chiwombankhanga+ chikuuluka pafupi m’mlengalenga,+ chikulankhula ndi mawu okweza kuti: “Tsoka, tsoka, tsoka+ kwa okhala padziko lapansi, chifukwa cha malipenga otsalawo, amene angelo atatuwo atsala pang’ono kuwaliza!”+
17 Ndinaonanso mngelo ataimirira padzuwa. Iye anafuula ndi mawu okweza kwa mbalame+ zonse zouluka chapafupi m’mlengalenga, kuti: “Bwerani kuno, dzasonkhaneni ku phwando lalikulu la Mulungu la chakudya chamadzulo,