Mateyu 25:46 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 46 Ndipo iwowa adzachoka kupita ku chiwonongeko chotheratu,+ koma olungama ku moyo wosatha.”+ 2 Atesalonika 1:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Amenewa adzawaweruza kuti alandire chilango+ cha chiwonongeko chamuyaya,+ kuwachotsa pamaso pa Ambuye ndi ku ulemerero wa mphamvu zake.+ Chivumbulutso 19:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Nthawi yomweyo, ananenanso kachiwiri kuti: “Tamandani Ya, anthu inu!+ Utsi wochokera kwa iye udzafuka kwamuyaya.”+
9 Amenewa adzawaweruza kuti alandire chilango+ cha chiwonongeko chamuyaya,+ kuwachotsa pamaso pa Ambuye ndi ku ulemerero wa mphamvu zake.+
3 Nthawi yomweyo, ananenanso kachiwiri kuti: “Tamandani Ya, anthu inu!+ Utsi wochokera kwa iye udzafuka kwamuyaya.”+