2 Samueli 16:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Ponyoza, Simeyi anali kunena kuti: “Choka, choka, munthu wa mlandu wamagazi+ ndi wopanda pake iwe!+ Salimo 62:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Iwo amapatsa munthu malangizo kuti amukope ndi kumutsitsa pamalo ake aulemu.+Bodza limawasangalatsa.+Iwo amadalitsa ndi pakamwa pawo, koma mumtima mwawo amatemberera.+ [Seʹlah.]
7 Ponyoza, Simeyi anali kunena kuti: “Choka, choka, munthu wa mlandu wamagazi+ ndi wopanda pake iwe!+
4 Iwo amapatsa munthu malangizo kuti amukope ndi kumutsitsa pamalo ake aulemu.+Bodza limawasangalatsa.+Iwo amadalitsa ndi pakamwa pawo, koma mumtima mwawo amatemberera.+ [Seʹlah.]