Mateyu 2:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Ndiyeno powatumiza ku Betelehemu, iye anawauza kuti: “Pitani mukam’funefune mwanayo mosamala, ndipo mukakam’peza mudzandidziwitse, kuti nanenso ndipite kukam’gwadira.”+
8 Ndiyeno powatumiza ku Betelehemu, iye anawauza kuti: “Pitani mukam’funefune mwanayo mosamala, ndipo mukakam’peza mudzandidziwitse, kuti nanenso ndipite kukam’gwadira.”+