Deuteronomo 13:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 ‘Pakati panu papezeka anthu opanda pake+ amene akufuna kupatutsa anthu mumzinda wawo,+ ponena kuti: “Tiyeni tikatumikire milungu ina,” milungu imene inu simunaidziwe,’ 1 Samueli 2:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Tsopano ana aamuna a Eli anali anthu opanda pake.+ Iwo anali kunyalanyaza Yehova.+ 1 Samueli 25:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Choncho mudziwe zimenezi ndi kuona zimene mungachite, chifukwa atsimikiza kudzetsa tsoka+ pa mbuyanga ndi onse a m’nyumba yake, pakuti mbuye wathu ndi munthu wopanda pake,+ sitingathe kulankhula naye.” Yobu 34:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Kodi munthu anganene kwa mfumu kuti, ‘Ndinu wopanda pake’?Kapena angauze anthu olemekezeka kuti, ‘Ndinu oipa’?+
13 ‘Pakati panu papezeka anthu opanda pake+ amene akufuna kupatutsa anthu mumzinda wawo,+ ponena kuti: “Tiyeni tikatumikire milungu ina,” milungu imene inu simunaidziwe,’
17 Choncho mudziwe zimenezi ndi kuona zimene mungachite, chifukwa atsimikiza kudzetsa tsoka+ pa mbuyanga ndi onse a m’nyumba yake, pakuti mbuye wathu ndi munthu wopanda pake,+ sitingathe kulankhula naye.”
18 Kodi munthu anganene kwa mfumu kuti, ‘Ndinu wopanda pake’?Kapena angauze anthu olemekezeka kuti, ‘Ndinu oipa’?+