1 Samueli 2:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Tsopano ana aamuna a Eli anali anthu opanda pake.+ Iwo anali kunyalanyaza Yehova.+ 1 Mafumu 21:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Ndiyeno mupeze anthu awiri+ opanda pake+ adzakhale patsogolo pake ndi kupereka umboni wotsutsana naye.+ Adzanene kuti, ‘Iwe watemberera Mulungu ndi mfumu!’+ Kenako mukamutulutse kunja ndi kum’ponya miyala kuti afe.”+ Yuda 19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Anthu amenewa ndiwo amayambitsa magawano,+ amachita zauchinyama,+ ndipo alibe mzimu wa Mulungu.+
10 Ndiyeno mupeze anthu awiri+ opanda pake+ adzakhale patsogolo pake ndi kupereka umboni wotsutsana naye.+ Adzanene kuti, ‘Iwe watemberera Mulungu ndi mfumu!’+ Kenako mukamutulutse kunja ndi kum’ponya miyala kuti afe.”+