Salimo 64:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Amaumirira kulankhula zoipa,+Amakambirana kuti atchere misampha.+Iwo amati: “Angaione ndani?”+ Salimo 119:110 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 110 Oipa anditchera msampha,+Koma ine sindinasochere ndi kuchoka pa malamulo anu.+ Luka 20:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 Ndiyeno ataonetsetsa zochita zake, anatuma aganyu mwachinsinsi kuti akadzionetse ngati olungama, n’cholinga choti akamukole+ m’mawu ake, kuti akamupereke ku boma ndi kwa bwanamkubwa.+
20 Ndiyeno ataonetsetsa zochita zake, anatuma aganyu mwachinsinsi kuti akadzionetse ngati olungama, n’cholinga choti akamukole+ m’mawu ake, kuti akamupereke ku boma ndi kwa bwanamkubwa.+