Mateyu 27:25 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 25 Atanena izi anthu onse anayankha kuti: “Magazi ake akhala pa ife ndi pa ana athu.”+ Machitidwe 3:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Chotero munapha Mtumiki Wamkulu wa moyo,+ koma Mulungu anamuukitsa kwa akufa, ndipo ife ndife mboni za choonadi chimenechi.+
15 Chotero munapha Mtumiki Wamkulu wa moyo,+ koma Mulungu anamuukitsa kwa akufa, ndipo ife ndife mboni za choonadi chimenechi.+