Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Deuteronomo 19:10
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 10 kuti musakhetse magazi a munthu wosalakwa+ pakati pa dziko lanu limene Yehova Mulungu wanu akukupatsani monga cholowa, kotero kuti musakhale ndi mlandu wa magazi.+

  • Yoswa 2:19
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 19 Aliyense amene adzatuluke pakhomo la nyumba yako kupita panja,+ magazi ake adzakhala pamutu pake. Ife tidzakhala opanda mlandu. Koma ngati aliyense amene adzakhalebe limodzi nawe m’nyumbamu adzaphedwe, magazi ake adzakhale pamutu pathu.

  • Machitidwe 5:28
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 28 kuti: “Tinakulamulani mwamphamvu+ kuti musadzaphunzitsenso m’dzina limeneli, koma taonani tsopano! Mwadzaza Yerusalemu yense ndi chiphunzitso chanuchi,+ ndipo mwatsimikiza mtima ndithu kuti mubweretse magazi+ a munthu ameneyu pa ife.”

  • 1 Atesalonika 2:15
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 15 amene anapha ngakhale Ambuye Yesu+ ndi aneneri+ ndi kuzunzanso ifeyo.+ Ndipo iwo sakukondweretsa Mulungu, koma akutsekereza zinthu zopindulitsa anthu onse.

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena