Genesis 4:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Ukasintha n’kuchita chabwino, sindikuyanja kodi?+ Koma ngati susintha kuti uchite chabwino, uchimo wamyata pakhomo kukudikirira, ndipo ukulakalaka kukudya.+ Kodi iweyo suugonjetsa?”+ Miyambo 11:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Kulungama kwa munthu wopanda cholakwa n’kumene kudzawongole njira yake,+ koma woipa adzagwera m’zoipa zakezo.+ Mateyu 7:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Momwemonso mtengo uliwonse wabwino umabala zipatso zabwino, koma mtengo uliwonse wovunda umabala zipatso zopanda pake.+ Agalatiya 6:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Musanyengedwe,+ Mulungu sapusitsika.+ Chilichonse chimene munthu wafesa, adzakololanso chomwecho.+
7 Ukasintha n’kuchita chabwino, sindikuyanja kodi?+ Koma ngati susintha kuti uchite chabwino, uchimo wamyata pakhomo kukudikirira, ndipo ukulakalaka kukudya.+ Kodi iweyo suugonjetsa?”+
5 Kulungama kwa munthu wopanda cholakwa n’kumene kudzawongole njira yake,+ koma woipa adzagwera m’zoipa zakezo.+
17 Momwemonso mtengo uliwonse wabwino umabala zipatso zabwino, koma mtengo uliwonse wovunda umabala zipatso zopanda pake.+