Mateyu 12:33 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 33 “Anthu inu mumachititsa mtengo ndi zipatso zake kukhala zabwino, kapena mumavunditsa mtengo ndi zipatso zake, chifukwa mtengo umadziwika ndi zipatso zake.+ Luka 6:43 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 43 “Kulibe mtengo wabwino umene ungabale chipatso chowola. Ndipo palibe mtengo wowola umene ungabale chipatso chabwino.+
33 “Anthu inu mumachititsa mtengo ndi zipatso zake kukhala zabwino, kapena mumavunditsa mtengo ndi zipatso zake, chifukwa mtengo umadziwika ndi zipatso zake.+
43 “Kulibe mtengo wabwino umene ungabale chipatso chowola. Ndipo palibe mtengo wowola umene ungabale chipatso chabwino.+