Mateyu 7:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Momwemonso mtengo uliwonse wabwino umabala zipatso zabwino, koma mtengo uliwonse wovunda umabala zipatso zopanda pake.+ Luka 6:43 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 43 “Kulibe mtengo wabwino umene ungabale chipatso chowola. Ndipo palibe mtengo wowola umene ungabale chipatso chabwino.+
17 Momwemonso mtengo uliwonse wabwino umabala zipatso zabwino, koma mtengo uliwonse wovunda umabala zipatso zopanda pake.+
43 “Kulibe mtengo wabwino umene ungabale chipatso chowola. Ndipo palibe mtengo wowola umene ungabale chipatso chabwino.+