Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • 1 Samueli 25:25
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 25 Chonde mbuyanga, musaganizire za Nabala, munthu wopanda pakeyu,+ chifukwa zochita zake ndi zogwirizana ndi dzina lake. Dzina lake ndi Nabala* ndipo ndi wopandadi nzeru.+ Koma ine kapolo wanu wamkazi sindinawaone anyamata amene inu mbuyanga munawatuma.

  • Mateyu 12:34
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 34 Ana a njoka inu,+ mungalankhule bwanji zinthu zabwino, pamene muli oipa?+ Pakuti pakamwa pamalankhula zosefukira mumtima.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena