Ekisodo 15:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Ndi mulungu wina uti amene angafanane nanu, inu Yehova?+Ndinu woyera kopambana, ndani angafanane ndi inu?+Ndinu woyenera kuopedwa+ ndi kukuimbirani nyimbo zotamanda.+ Inu ndinu wochita zodabwitsa.+ Salimo 71:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Chilungamo chanu, inu Mulungu chafika kumwamba.+Tikanena za zinthu zazikulu zimene munachita,+Inu Mulungu, ndani angafanane ndi inu?+
11 Ndi mulungu wina uti amene angafanane nanu, inu Yehova?+Ndinu woyera kopambana, ndani angafanane ndi inu?+Ndinu woyenera kuopedwa+ ndi kukuimbirani nyimbo zotamanda.+ Inu ndinu wochita zodabwitsa.+
19 Chilungamo chanu, inu Mulungu chafika kumwamba.+Tikanena za zinthu zazikulu zimene munachita,+Inu Mulungu, ndani angafanane ndi inu?+