Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • 1 Samueli 24:5
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 5 Koma pambuyo pake, Davide anavutika mumtima mwake+ chifukwa chakuti anali atadula kansalu m’munsi mwa malaya akunja odula manja a Sauli.

  • Machitidwe 2:37
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 37 Tsopano iwo atamva mawu amenewa, anavutika kwambiri mumtima,+ ndipo anafunsa Petulo ndi atumwi enawo kuti: “Amuna inu, abale athu, tichite chiyani pamenepa?”+

  • Aroma 2:15
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 15 Amenewa ndiwo amasonyeza kuti mfundo za m’chilamulo zinalembedwa m’mitima mwawo,+ pamene chikumbumtima chawo+ chimachitira umboni pamodzi ndi iwowo, ndipo maganizo awo amawatsutsa+ ngakhalenso kuwavomereza.

  • 2 Akorinto 7:10
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 10 Kumva chisoni mogwirizana ndi chifuniro cha Mulungu kumachititsa munthu kulapa ndi kupeza chipulumutso, zimene munthu sangadandaule nazo.+ Koma chisoni cha dziko chimabweretsa imfa.+

  • 1 Yohane 3:20
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 20 pa chilichonse chimene mitima yathu ingatitsutse,+ chifukwa Mulungu ndi wamkulu kuposa mitima yathu ndipo amadziwa zonse.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena