Luka 12:30 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 30 Pakuti zonsezi ndi zinthu zimene anthu a mitundu ina a m’dzikoli amazifunafuna mwakhama, koma Atate wanu amadziwa kuti zinthu zonsezi n’zofunika kwa inu.+ Aheberi 4:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Palibe cholengedwa chimene Mulungu sangathe kuchiona.+ Chifukwa kwa iye zinthu zonse zili poonekera ndipo amatha kuziona bwinobwino. Ndipotu ife tikuyenera kudzayankha pa zochita zathu kwa Mulungu amene amaona zonseyo.+
30 Pakuti zonsezi ndi zinthu zimene anthu a mitundu ina a m’dzikoli amazifunafuna mwakhama, koma Atate wanu amadziwa kuti zinthu zonsezi n’zofunika kwa inu.+
13 Palibe cholengedwa chimene Mulungu sangathe kuchiona.+ Chifukwa kwa iye zinthu zonse zili poonekera ndipo amatha kuziona bwinobwino. Ndipotu ife tikuyenera kudzayankha pa zochita zathu kwa Mulungu amene amaona zonseyo.+