2 Samueli 12:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Pamenepo Davide anauza+ Natani kuti: “Ndachimwira Yehova.”+ Ndiyeno Natani anauza Davide kuti: “Yehova wakukhululukira tchimo lako+ ndipo suufa.+ 1 Mbiri 21:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Davide ataona zimenezo, anauza Mulungu woona kuti: “Ndachimwa+ kwambiri pochita zimene ndachitazi. Tsopano, chonde, khululukani cholakwa cha ine mtumiki wanu,+ pakuti ndachita chinthu chopusa kwambiri.”+
13 Pamenepo Davide anauza+ Natani kuti: “Ndachimwira Yehova.”+ Ndiyeno Natani anauza Davide kuti: “Yehova wakukhululukira tchimo lako+ ndipo suufa.+
8 Davide ataona zimenezo, anauza Mulungu woona kuti: “Ndachimwa+ kwambiri pochita zimene ndachitazi. Tsopano, chonde, khululukani cholakwa cha ine mtumiki wanu,+ pakuti ndachita chinthu chopusa kwambiri.”+