1 Mbiri 21:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Kenako Davide anauza Mulungu woona kuti: “Ndachimwa+ kwambiri pochita zimenezi. Chonde ndikhululukireni tchimo langa ine mtumiki wanu,+ chifukwa ndachita zopusa kwambiri.”+
8 Kenako Davide anauza Mulungu woona kuti: “Ndachimwa+ kwambiri pochita zimenezi. Chonde ndikhululukireni tchimo langa ine mtumiki wanu,+ chifukwa ndachita zopusa kwambiri.”+