1 Mbiri 21:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Davide ataona zimenezo, anauza Mulungu woona kuti: “Ndachimwa+ kwambiri pochita zimene ndachitazi. Tsopano, chonde, khululukani cholakwa cha ine mtumiki wanu,+ pakuti ndachita chinthu chopusa kwambiri.”+
8 Davide ataona zimenezo, anauza Mulungu woona kuti: “Ndachimwa+ kwambiri pochita zimene ndachitazi. Tsopano, chonde, khululukani cholakwa cha ine mtumiki wanu,+ pakuti ndachita chinthu chopusa kwambiri.”+