Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • 1 Samueli 13:13
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 13 Pamenepo Samueli anauza Sauli kuti: “Wachita chinthu chopusa.+ Sunatsatire lamulo+ limene Yehova Mulungu wako anakupatsa.+ Ukanatsatira lamulo limeneli, Yehova akanalimbitsa ufumu wako pa Isiraeli mpaka kalekale.

  • Salimo 107:17
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 17 Anthu amene anali opusa chifukwa cha njira yawo yophwanya malamulo,+

      Komanso chifukwa cha zolakwa zawo, pamapeto pake anadzibweretsera masautso.+

  • Mlaliki 10:1
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 10 Ntchentche zakufa n’zimene zimachititsa mafuta onunkhira oyengedwa bwino+ kuwola ndi kuyamba kununkha. Momwemonso uchitsiru pang’ono umawononga mbiri ya munthu amene akulemekezedwa chifukwa cha nzeru ndi ulemerero wake.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena