Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Numeri 11:33
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 33 Nyamayo ikadali m’kamwa mwawo,+ asanaitafune, mkwiyo wa Yehova unawayakira+ anthuwo. Ndipo Yehova anayamba kuwakantha anthuwo n’kuwapha ambiri.+

  • Salimo 38:5
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    •  5 Zilonda zanga zanunkha ndi kunyeka,

      Chifukwa cha kupusa kwanga.+

  • Yeremiya 2:19
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 19 Uphunzirepo kanthu pa kuipa kwako+ ndipo zochita zako zosakhulupirika zikudzudzule.+ Dziwa izi, ndipo ona kuti kusiya kwako Yehova Mulungu wako ndi chinthu choipa ndi chowawa.+ Iwe sundiopa ine,’+ watero Yehova wa makamu, Ambuye Wamkulu Koposa.+

  • Agalatiya 6:7
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 7 Musanyengedwe,+ Mulungu sapusitsika.+ Chilichonse chimene munthu wafesa, adzakololanso chomwecho.+

  • 2 Petulo 2:13
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 13 ndipo akudzilakwira okha+ monga mphoto yawo ya kuchita zoipa.+

      Iwo amaona kuti kuchita masana zinthu zokhutiritsa chilakolako cha thupi lawo n’kosangalatsa.+ Anthu amenewa ali ngati mawanga ndi zilema pakati panu, ndipo amakondwera kwadzaoneni akamakuphunzitsani zinthu zonyenga pamene akudya nanu limodzi.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena