Numeri 11:33 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 33 Koma nyamayo idakali mʼkamwa mwawo, asanaitafune nʼkomwe, mkwiyo wa Yehova unayakira anthuwo. Ndipo Yehova anayamba kuwalanga moti anthu ambiri anaphedwa.+ Numeri Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 11:33 Nsanja ya Olonda,3/1/1995, tsa. 16
33 Koma nyamayo idakali mʼkamwa mwawo, asanaitafune nʼkomwe, mkwiyo wa Yehova unayakira anthuwo. Ndipo Yehova anayamba kuwalanga moti anthu ambiri anaphedwa.+