Numeri 11:33 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 33 Nyamayo ikadali m’kamwa mwawo,+ asanaitafune, mkwiyo wa Yehova unawayakira+ anthuwo. Ndipo Yehova anayamba kuwakantha anthuwo n’kuwapha ambiri.+ Numeri Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 11:33 Nsanja ya Olonda,3/1/1995, tsa. 16
33 Nyamayo ikadali m’kamwa mwawo,+ asanaitafune, mkwiyo wa Yehova unawayakira+ anthuwo. Ndipo Yehova anayamba kuwakantha anthuwo n’kuwapha ambiri.+