Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Salimo 36:7
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    •  7 Inu Mulungu, kukoma mtima kwanu kosatha ndi kwamtengo wapatali!+

      Ndipo ana a anthu amabisala mu mthunzi wa mapiko anu.+

  • Salimo 62:12
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 12 Komanso kukoma mtima kosatha ndi kwanu, inu Yehova,+

      Pakuti inu mumabwezera aliyense mogwirizana ndi ntchito zake.+

  • Salimo 103:9
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    •  9 Iye sadzakhalira kutiimba mlandu nthawi zonse chifukwa cha zolakwa zathu,+

      Kapena kutisungira mkwiyo mpaka kalekale.+

  • Yesaya 57:16
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 16 Pakuti ine sindidzatsutsana nanu mpaka kalekale, ndiponso sindidzakhala wokwiya mpaka kalekale.+ Popeza chifukwa cha ine, mzimu wa munthu ukhoza kufooka,+ ngakhalenso zinthu zopuma zimene ineyo ndinapanga.+

  • Maliro 3:22
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 22 Chifukwa cha kukoma mtima kosatha+ kwa Yehova, ife sitinafafanizidwe,+ ndipo chifundo chake sichidzatha.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena