Yesaya 57:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Pakuti ine sindidzatsutsana nanu mpaka kalekale, ndiponso sindidzakhala wokwiya mpaka kalekale.+ Popeza chifukwa cha ine, mzimu wa munthu ukhoza kufooka,+ ngakhalenso zinthu zopuma zimene ineyo ndinapanga.+
16 Pakuti ine sindidzatsutsana nanu mpaka kalekale, ndiponso sindidzakhala wokwiya mpaka kalekale.+ Popeza chifukwa cha ine, mzimu wa munthu ukhoza kufooka,+ ngakhalenso zinthu zopuma zimene ineyo ndinapanga.+