Numeri 16:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 Anthuwo atamva zimenezi anagwada n’kuwerama mpaka nkhope zawo pansi, n’kunena kuti: “Chonde Mulungu, inu Mulungu amene amapereka moyo kwa zamoyo zonse,+ kodi kuchimwa kwa munthu mmodzi yekha n’kumene mungapsere mtima khamu lonseli?”+ Yobu 34:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Akaika mtima wake pa munthu aliyense,Akatenga mzimu* ndi mpweya wa munthuyo,+ Mlaliki 12:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Kenako fumbi lidzabwerera kunthaka+ kumene linali, ndipo mzimu*+ udzabwerera kwa Mulungu woona+ amene anaupereka.+
22 Anthuwo atamva zimenezi anagwada n’kuwerama mpaka nkhope zawo pansi, n’kunena kuti: “Chonde Mulungu, inu Mulungu amene amapereka moyo kwa zamoyo zonse,+ kodi kuchimwa kwa munthu mmodzi yekha n’kumene mungapsere mtima khamu lonseli?”+
14 Akaika mtima wake pa munthu aliyense,Akatenga mzimu* ndi mpweya wa munthuyo,+ Mlaliki 12:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Kenako fumbi lidzabwerera kunthaka+ kumene linali, ndipo mzimu*+ udzabwerera kwa Mulungu woona+ amene anaupereka.+
7 Kenako fumbi lidzabwerera kunthaka+ kumene linali, ndipo mzimu*+ udzabwerera kwa Mulungu woona+ amene anaupereka.+