Salimo 31:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Ubwino wanu,+ umene mwasungira anthu okuopani ndi wochuluka kwambiri!+Ubwino umenewu mwapereka kwa anthu othawira kwa inu.Mwaupereka kwa iwo, ana a anthu akuona.+ Mika 7:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Kodi pali Mulungu winanso wofanana ndi inu+ amene amakhululukira zolakwa+ ndi machimo a anthu ake otsala omwe ndi cholowa chake?+ Inu simudzakhalabe wokwiya mpaka kalekale, pakuti kusonyeza kukoma mtima kosatha kumakusangalatsani.+
19 Ubwino wanu,+ umene mwasungira anthu okuopani ndi wochuluka kwambiri!+Ubwino umenewu mwapereka kwa anthu othawira kwa inu.Mwaupereka kwa iwo, ana a anthu akuona.+
18 Kodi pali Mulungu winanso wofanana ndi inu+ amene amakhululukira zolakwa+ ndi machimo a anthu ake otsala omwe ndi cholowa chake?+ Inu simudzakhalabe wokwiya mpaka kalekale, pakuti kusonyeza kukoma mtima kosatha kumakusangalatsani.+