Rute 2:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Yehova akudalitse chifukwa cha zimene wachita,+ ndipo Yehova, Mulungu wa Isiraeli akufupe mokwanira.+ Iye amene m’mapiko mwake wathawiramo ndi kupezamo chitetezo.”+ Salimo 17:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Ndisungeni monga mwana wa diso,+Ndibiseni mumthunzi wa mapiko anu,+ Salimo 91:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Adzakutchinjiriza ndi mapiko ake,+Udzathawira pansi pa mapiko ake.+Choonadi chake+ chidzakhala chishango chako+ chachikulu ndi malo ako achitetezo.
12 Yehova akudalitse chifukwa cha zimene wachita,+ ndipo Yehova, Mulungu wa Isiraeli akufupe mokwanira.+ Iye amene m’mapiko mwake wathawiramo ndi kupezamo chitetezo.”+
8 Ndisungeni monga mwana wa diso,+Ndibiseni mumthunzi wa mapiko anu,+ Salimo 91:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Adzakutchinjiriza ndi mapiko ake,+Udzathawira pansi pa mapiko ake.+Choonadi chake+ chidzakhala chishango chako+ chachikulu ndi malo ako achitetezo.
4 Adzakutchinjiriza ndi mapiko ake,+Udzathawira pansi pa mapiko ake.+Choonadi chake+ chidzakhala chishango chako+ chachikulu ndi malo ako achitetezo.