Mateyu 15:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 Izi n’zimene zimaipitsa munthu, koma kudya chakudya osasamba m’manja sikuipitsa munthu.”+ Aroma 1:28 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 28 Ndiponso monga mmene iwo sanafunire kumudziwa Mulungu molondola,+ iye anawasiya ndi maganizo awo oipa,+ kuti azichita zinthu zosayenerazo,+
28 Ndiponso monga mmene iwo sanafunire kumudziwa Mulungu molondola,+ iye anawasiya ndi maganizo awo oipa,+ kuti azichita zinthu zosayenerazo,+