Genesis 44:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Tsopano Yuda anayandikira kwa Yosefe n’kunena kuti: “Chonde mbuyanga, ndapota nanu. Lolani kuti kapolo wanune ndinene mawu amodzi okha.+ Chonde musandipsere mtima,+ pakuti inu muli ngati Farao+ yemwe.
18 Tsopano Yuda anayandikira kwa Yosefe n’kunena kuti: “Chonde mbuyanga, ndapota nanu. Lolani kuti kapolo wanune ndinene mawu amodzi okha.+ Chonde musandipsere mtima,+ pakuti inu muli ngati Farao+ yemwe.