Yobu 30:28 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 28 Ndinayendayenda mwachisoni+ pamene kunalibe kuwala.Ndinaimirira mumpingo, ndipo ndinkangofuula popempha thandizo. Salimo 42:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Ndidzauza Mulungu, thanthwe langa kuti:+“N’chifukwa chiyani mwandiiwala?+Ndikuyenderanji wachisoni chifukwa choponderezedwa ndi mdani wanga?”+
28 Ndinayendayenda mwachisoni+ pamene kunalibe kuwala.Ndinaimirira mumpingo, ndipo ndinkangofuula popempha thandizo.
9 Ndidzauza Mulungu, thanthwe langa kuti:+“N’chifukwa chiyani mwandiiwala?+Ndikuyenderanji wachisoni chifukwa choponderezedwa ndi mdani wanga?”+