Salimo 38:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Ndasokonezeka ndipo ndawerama kwambiri chifukwa cha chisoni changa.+Ndayenda uku ndi uku tsiku lonse ndili wachisoni.+ Salimo 42:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Ndidzauza Mulungu, thanthwe langa kuti:+“N’chifukwa chiyani mwandiiwala?+Ndikuyenderanji wachisoni chifukwa choponderezedwa ndi mdani wanga?”+ Salimo 43:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Pakuti inu ndinu Mulungu wanga, ndinu malo anga achitetezo.+N’chifukwa chiyani mwanditaya?Ndikuyenderanji wachisoni chifukwa choponderezedwa ndi mdani wanga?+
6 Ndasokonezeka ndipo ndawerama kwambiri chifukwa cha chisoni changa.+Ndayenda uku ndi uku tsiku lonse ndili wachisoni.+
9 Ndidzauza Mulungu, thanthwe langa kuti:+“N’chifukwa chiyani mwandiiwala?+Ndikuyenderanji wachisoni chifukwa choponderezedwa ndi mdani wanga?”+
2 Pakuti inu ndinu Mulungu wanga, ndinu malo anga achitetezo.+N’chifukwa chiyani mwanditaya?Ndikuyenderanji wachisoni chifukwa choponderezedwa ndi mdani wanga?+