Salimo 35:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Chifukwa cha mnzanga ndiponso m’bale wanga,+Ndinamva chisoni kwambiri ngati munthu wolira maliro a mayi ake.+Ndinawerama chifukwa cha chisoni.
14 Chifukwa cha mnzanga ndiponso m’bale wanga,+Ndinamva chisoni kwambiri ngati munthu wolira maliro a mayi ake.+Ndinawerama chifukwa cha chisoni.