Genesis 24:67 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 67 Zitatero, Isaki analowa ndi mkaziyo m’hema wa Sara, mayi ake.+ Umu ndi mmene Isaki anatengera Rabeka kukhala mkazi wake.+ Iye anam’konda kwambiri,+ ndipo anatonthozedwa pambuyo pa imfa ya mayi ake.+
67 Zitatero, Isaki analowa ndi mkaziyo m’hema wa Sara, mayi ake.+ Umu ndi mmene Isaki anatengera Rabeka kukhala mkazi wake.+ Iye anam’konda kwambiri,+ ndipo anatonthozedwa pambuyo pa imfa ya mayi ake.+