Genesis 24:67 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 67 Ndiyeno Isaki analowa ndi mkaziyo mutenti ya Sara, mayi ake.+ Choncho Isaki anatenga Rabeka kukhala mkazi wake. Iye anamʼkonda kwambiri,+ ndipo zimenezi zinamutonthoza pambuyo pa imfa ya mayi ake.+ Genesis Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 24:67 Nsanja ya Olonda (Yogawira),No. 3 2016, tsa. 15 Nsanja ya Olonda,7/1/1989, tsa. 28
67 Ndiyeno Isaki analowa ndi mkaziyo mutenti ya Sara, mayi ake.+ Choncho Isaki anatenga Rabeka kukhala mkazi wake. Iye anamʼkonda kwambiri,+ ndipo zimenezi zinamutonthoza pambuyo pa imfa ya mayi ake.+