Genesis 24:67 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 67 Zitatero, Isaki analowa ndi mkaziyo m’hema wa Sara, mayi ake.+ Umu ndi mmene Isaki anatengera Rabeka kukhala mkazi wake.+ Iye anam’konda kwambiri,+ ndipo anatonthozedwa pambuyo pa imfa ya mayi ake.+ Genesis Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 24:67 Nsanja ya Olonda (Yogawira),No. 3 2016, tsa. 15 Nsanja ya Olonda,7/1/1989, tsa. 28
67 Zitatero, Isaki analowa ndi mkaziyo m’hema wa Sara, mayi ake.+ Umu ndi mmene Isaki anatengera Rabeka kukhala mkazi wake.+ Iye anam’konda kwambiri,+ ndipo anatonthozedwa pambuyo pa imfa ya mayi ake.+