Salimo 3:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Inu Yehova, nʼchifukwa chiyani adani anga achuluka chonchi?+ Nʼchifukwa chiyani anthu ambiri akundiukira?+ Masalimo Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 3:1 Nsanja ya Olonda,5/15/2011, tsa. 28
3 Inu Yehova, nʼchifukwa chiyani adani anga achuluka chonchi?+ Nʼchifukwa chiyani anthu ambiri akundiukira?+