Ekisodo 15:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Mdaniyo anati, ‘Ndiwathamangira,+ ndi kuwapeza!+Ndigawa chuma chawo.+ Pamenepo moyo wanga ukhutira ndi zimene ndawachita!Ndisolola lupanga langa! Dzanja langa liwawononga!’+ Yoswa 24:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Pamene ndinali kutulutsa makolo anu ku Iguputo,+ atatsala pang’ono kufika kunyanja, Aiguputo anawathamangira+ ndi magaleta ankhondo ndiponso amuna okwera pamahatchi, mpaka ku Nyanja Yofiira.
9 Mdaniyo anati, ‘Ndiwathamangira,+ ndi kuwapeza!+Ndigawa chuma chawo.+ Pamenepo moyo wanga ukhutira ndi zimene ndawachita!Ndisolola lupanga langa! Dzanja langa liwawononga!’+
6 Pamene ndinali kutulutsa makolo anu ku Iguputo,+ atatsala pang’ono kufika kunyanja, Aiguputo anawathamangira+ ndi magaleta ankhondo ndiponso amuna okwera pamahatchi, mpaka ku Nyanja Yofiira.