Ekisodo 12:37 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 37 Pamenepo ana a Isiraeli ananyamuka ku Ramese+ kupita ku Sukoti.+ Amuna amphamvu oyenda pansi analipo pafupifupi 600,000, osawerengera ana.+ Mika 6:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Ine ndinakutulutsani m’dziko la Iguputo,+ ndipo ndinakuwombolani m’nyumba ya akapolo.+ Ndinakutumizirani Mose, Aroni ndi Miriamu kuti akutsogolereni.+
37 Pamenepo ana a Isiraeli ananyamuka ku Ramese+ kupita ku Sukoti.+ Amuna amphamvu oyenda pansi analipo pafupifupi 600,000, osawerengera ana.+
4 Ine ndinakutulutsani m’dziko la Iguputo,+ ndipo ndinakuwombolani m’nyumba ya akapolo.+ Ndinakutumizirani Mose, Aroni ndi Miriamu kuti akutsogolereni.+