Ekisodo 14:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Motero Aiguputo anali kuwathamangira, ndipo magaleta onse a Farao, asilikali apamahatchi+ ndi magulu ake ankhondo anawayandikira. Aisiraeliwo anali atamanga msasa m’mphepete mwa nyanja, pafupi ndi Pihahiroti moyang’anizana ndi Baala-zefoni.+
9 Motero Aiguputo anali kuwathamangira, ndipo magaleta onse a Farao, asilikali apamahatchi+ ndi magulu ake ankhondo anawayandikira. Aisiraeliwo anali atamanga msasa m’mphepete mwa nyanja, pafupi ndi Pihahiroti moyang’anizana ndi Baala-zefoni.+