Salimo 14:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Wopusa amanena mumtima mwake kuti:“Kulibe Yehova.”+Anthu oterewa amachita zoipa,+ ndipo amachita zinthu zonyansa.Palibe amene akuchita zabwino.+ Salimo 53:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 53 Wopusa amanena mumtima mwake kuti:“Kulibe Yehova.”+Anthu oterewa amachita zoipa, ndipo amachita zinthu zonyansa zogwirizana ndi kupanda chilungamo kwawo.+Palibe amene akuchita zabwino.+ Zefaniya 1:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 “Pa nthawi imeneyo ndidzafufuza ndi nyale mu Yerusalemu mosamala kwambiri,+ ndipo ndidzalanga anthu amene akukhala mosatekeseka ngati vinyo amene nsenga zake zakhazikika pansi.+ M’mitima yawo, anthu amenewa akunena kuti, ‘Yehova sadzachita zabwino kapena kuchita zoipa.’+
14 Wopusa amanena mumtima mwake kuti:“Kulibe Yehova.”+Anthu oterewa amachita zoipa,+ ndipo amachita zinthu zonyansa.Palibe amene akuchita zabwino.+
53 Wopusa amanena mumtima mwake kuti:“Kulibe Yehova.”+Anthu oterewa amachita zoipa, ndipo amachita zinthu zonyansa zogwirizana ndi kupanda chilungamo kwawo.+Palibe amene akuchita zabwino.+
12 “Pa nthawi imeneyo ndidzafufuza ndi nyale mu Yerusalemu mosamala kwambiri,+ ndipo ndidzalanga anthu amene akukhala mosatekeseka ngati vinyo amene nsenga zake zakhazikika pansi.+ M’mitima yawo, anthu amenewa akunena kuti, ‘Yehova sadzachita zabwino kapena kuchita zoipa.’+