Ekisodo 9:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Kodi ukudzikwezabe pa anthu anga, pokana kuwalola kuti achoke?+ Ekisodo 16:28 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 28 Choncho Yehova anauza Mose kuti: “Kodi anthu inu mudzakanabe kusunga malamulo ndi malangizo anga kufikira liti?+ Miyambo 18:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Munthu asanagwe, mtima wake umadzikweza,+ ndipo asanapeze ulemerero, amadzichepetsa.+ Yesaya 2:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Maso odzikuza a munthu wochokera kufumbi adzatsika, ndipo anthu odzikweza adzawerama.+ Yehova yekha ndi amene adzakwezedwe pamwamba m’tsiku limenelo.+ Yeremiya 13:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 “Uza mfumu ndi mayi a mfumu+ kuti, ‘Khalani pamalo apansi,+ pakuti chisoti chanu chaulemerero chidzachotsedwa pamutu panu ndi kuikidwa pansi.’+
28 Choncho Yehova anauza Mose kuti: “Kodi anthu inu mudzakanabe kusunga malamulo ndi malangizo anga kufikira liti?+
11 Maso odzikuza a munthu wochokera kufumbi adzatsika, ndipo anthu odzikweza adzawerama.+ Yehova yekha ndi amene adzakwezedwe pamwamba m’tsiku limenelo.+
18 “Uza mfumu ndi mayi a mfumu+ kuti, ‘Khalani pamalo apansi,+ pakuti chisoti chanu chaulemerero chidzachotsedwa pamutu panu ndi kuikidwa pansi.’+