Numeri 14:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Ndiyeno Yehova analankhula ndi Mose kuti: “Kodi anthu awa apitiriza kundinyoza kufikira liti?+ Kodi adzayamba liti kundikhulupirira pambuyo pa zizindikiro zonse zimene ndachita pakati pawo?+ 2 Mafumu 17:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Koma iwo sanamvere. M’malomwake anaumitsa makosi awo,+ ngati mmene makolo awo anaumitsira makosi awo. Makolo awowo sanasonyeze chikhulupiriro+ mwa Yehova Mulungu wawo. Salimo 78:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Iwo sanasunge pangano la Mulungu,+Ndipo anakana kutsatira chilamulo chake.+ Salimo 81:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Haa! Zikanakhala bwino ngati anthu anga akanandimvera,+Zikanakhala bwino ngati Isiraeli akanayenda m’njira zanga.+ Salimo 106:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Koma mofulumira anaiwala ntchito zake,+Iwo sanayembekezere malangizo ake.+ Luka 16:31 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 31 Koma iye anamuuza kuti, ‘Ngati sakumvera Zolemba za Mose+ ndi Zolemba za aneneri, sangathekebe ngakhale wina atauka kwa akufa.’”
11 Ndiyeno Yehova analankhula ndi Mose kuti: “Kodi anthu awa apitiriza kundinyoza kufikira liti?+ Kodi adzayamba liti kundikhulupirira pambuyo pa zizindikiro zonse zimene ndachita pakati pawo?+
14 Koma iwo sanamvere. M’malomwake anaumitsa makosi awo,+ ngati mmene makolo awo anaumitsira makosi awo. Makolo awowo sanasonyeze chikhulupiriro+ mwa Yehova Mulungu wawo.
13 Haa! Zikanakhala bwino ngati anthu anga akanandimvera,+Zikanakhala bwino ngati Isiraeli akanayenda m’njira zanga.+
31 Koma iye anamuuza kuti, ‘Ngati sakumvera Zolemba za Mose+ ndi Zolemba za aneneri, sangathekebe ngakhale wina atauka kwa akufa.’”