Deuteronomo 32:29 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 29 Akanakhala anzeru,+ akanaganizira mozama zimenezi.+Akanalingalira kuti ziwathera bwanji.+ Yesaya 48:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Zingakhale bwino kwambiri mutamvera malamulo anga!+ Mukatero mtendere wanu udzakhala ngati mtsinje,+ ndipo chilungamo chanu chidzakhala ngati mafunde a m’nyanja.+
18 Zingakhale bwino kwambiri mutamvera malamulo anga!+ Mukatero mtendere wanu udzakhala ngati mtsinje,+ ndipo chilungamo chanu chidzakhala ngati mafunde a m’nyanja.+