Yeremiya 2:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Uphunzirepo kanthu pa kuipa kwako+ ndipo zochita zako zosakhulupirika zikudzudzule.+ Dziwa izi, ndipo ona kuti kusiya kwako Yehova Mulungu wako ndi chinthu choipa ndi chowawa.+ Iwe sundiopa ine,’+ watero Yehova wa makamu, Ambuye Wamkulu Koposa.+ Maliro 1:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Zovala+ zake ndi zodetsedwa. Iye sanaganizire za tsogolo+ lake.Wagwa modabwitsa ndipo alibe womutonthoza.+Inu Yehova, onani kusautsika+ kwanga, pakuti mdani wanga akudzitukumula.+
19 Uphunzirepo kanthu pa kuipa kwako+ ndipo zochita zako zosakhulupirika zikudzudzule.+ Dziwa izi, ndipo ona kuti kusiya kwako Yehova Mulungu wako ndi chinthu choipa ndi chowawa.+ Iwe sundiopa ine,’+ watero Yehova wa makamu, Ambuye Wamkulu Koposa.+
9 Zovala+ zake ndi zodetsedwa. Iye sanaganizire za tsogolo+ lake.Wagwa modabwitsa ndipo alibe womutonthoza.+Inu Yehova, onani kusautsika+ kwanga, pakuti mdani wanga akudzitukumula.+