Yobu 9:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Iye ali ndi mtima wanzeru ndiponso mphamvu zambiri.+Ndani angachite naye makani,* koma osavulala?+ Yesaya 37:23 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 23 Kodi ndani amene iwe wamutonza+ ndi kumulankhula monyoza?+Ndipo ndani amene iwe wam’kwezera mawu,+Ndi kum’kwezera maso ako m’mwamba?+Ndi Woyera wa Isiraeli!+
23 Kodi ndani amene iwe wamutonza+ ndi kumulankhula monyoza?+Ndipo ndani amene iwe wam’kwezera mawu,+Ndi kum’kwezera maso ako m’mwamba?+Ndi Woyera wa Isiraeli!+