Salimo 26:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Pakuti kukoma mtima kwanu kosatha kuli pamaso panga.Ine ndayenda m’choonadi chanu.+ Salimo 40:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Chilungamo chanu sindinachibise mumtima mwanga.+Ndinalengeza za kukhulupirika kwanu ndi chipulumutso chanu.+Sindinabise kukoma mtima kwanu kosatha ndi choonadi chanu mumpingo waukulu.”+ Salimo 63:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Pakuti kukoma mtima kwanu kosatha n’kwabwino kuposa moyo,+Milomo yanga idzakuyamikirani.+
10 Chilungamo chanu sindinachibise mumtima mwanga.+Ndinalengeza za kukhulupirika kwanu ndi chipulumutso chanu.+Sindinabise kukoma mtima kwanu kosatha ndi choonadi chanu mumpingo waukulu.”+