Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Salimo 100:3
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    •  3 Dziwani kuti Yehova ndi Mulungu.+

      Iye ndi amene anatipanga, sitinadzipange tokha.+

      Ndife anthu ake ndi nkhosa zimene akuweta.+

  • Yesaya 43:15
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 15 Ine ndine Yehova, Woyera wanu,+ Mlengi wa Isiraeli+ ndiponso Mfumu yanu.”+

  • Aefeso 2:10
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 10 Pakuti ndife ntchito ya manja ake,+ ndipo tinalengedwa+ mogwirizana+ ndi Khristu Yesu kuti tichite ntchito zabwino,+ zimene Mulungu anakonzeratu+ kuti tiyendemo.

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena